Nkhani

Apolisi ayamba kuchititsa maphunziro

Apolisi m’boma la Salima ati ayamba kuchita maphunziro a okhudza umoyo wa anthu, chisamaliro cha ana, chitetezo cha m’mudzi komanso malingaliro a ngwiro. Inspector Rita Lazalo kuchokera ku nthambi yoona za chitetezo cha m’mudzi komanso kuthetsa nkhanza ati maphunzirowa akuchitika tsiku ndi tsiku kuti anthu akhale otetezeka komanso odziwa maufulu…
Read More

Alonjeza Kupititsa Chitukuko Patsogolo

Ngati njira imodzi yolimbikitsa chipani cha DPP m’dera lapakati m’boma la salima, a Symon Vuwa Kaunda omwe adaimira chipanichi m’derali ngati phungu alonjeza kugwira ntchito ndiotsatira chipanichi pofuna kupititsa patsogolo chitukoko m’delari. Poyankhula pa mkumano omwe anali nawo ndi otsatira chipanichi lachinayi, a Kaunda ati aika ndondomeko monga kutukura masewero,…
Read More

About Us

Love Holdings Limited is an umbrella organization committed to bridging communication and action for development. We combine trusted community broadcasting with practical agricultural solutions to create measurable social and economic impact.

Salima, Malawi