Apolisi ayamba kuchititsa maphunziro
Apolisi m’boma la Salima ati ayamba kuchita maphunziro a okhudza umoyo wa anthu, chisamaliro cha ana, chitetezo cha m’mudzi komanso malingaliro a ngwiro. Inspector Rita Lazalo kuchokera ku nthambi yoona za chitetezo cha m’mudzi komanso kuthetsa nkhanza ati maphunzirowa akuchitika tsiku ndi tsiku kuti anthu akhale otetezeka komanso odziwa maufulu…




